WIRE โ€” By Pickson Chipeso Lilongwe, June 26, Mana: Bungwe la Malawi Enterprise Development Fund (MEDF) Limited lachenjeza a Malawi kuti akhale tcheru ndi anthu omwe akudziyesa kuti ndi ogwira ntchito ku bungweli ndikugawa mafomu achinyengo a ngongole, kutsatira kuyambiranso kwa kupereka ngongole. Malingana ndi kalata yomwe bunweli latulutsa pa 26 Juni 2026 ndipo wsayinila ndi Mkulu

"We aggregate wires to encourage regional discovery, sending readers directly back to the original source to explore full coverage."

This is a normalized overview of the breaking feed event. The complete, official release detailing all points, background context, and statements remains hosted by the original publisher.